Eksodo 31:5 - Buku Lopatulika5 ndi kuzokota miyala yoikika, ndi kozokota mtengo, kuchita ntchito zilizonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 ndi kuzokota miyala yoikika, ndi kozokota mtengo, kuchita ntchito zilizonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Akudziŵanso kuzokota miyala yogwira nayo ntchito, kujoba mitengo, ndi kuchita zaluso zonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 kusema ndi kuyika miyala yokongola, kukonza zinthu zamatabwa ndiponso kugwira ntchito ina iliyonse yamanja. Onani mutuwo |