Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 31:4 - Buku Lopatulika

4 kulingirira ntchito zaluso, kuchita ndi golide ndi siliva ndi mkuwa,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 kulingirira ntchito zaluso, kuchita ndi golide ndi siliva ndi mkuwa,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 kulemba mapulani a ntchito zaluso ndi kugwira ntchito ndi golide, siliva ndi mkuŵa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Kulemba ndondomeko ya ntchito zaluso ndi kupanga zinthu zagolide, zasiliva ndi zamkuwa,

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 31:4
8 Mawu Ofanana  

Iyeyo anali mwana wake wa mkazi wamasiye wa fuko la Nafutali, atate wake anali munthu wa ku Tiro, mfundi wamkuwa; ndipo iye anadzala ndi nzeru ndi luntha ndi luso kugwira ntchito zonse za mkuwa. Ndipo anadza kwa mfumu Solomoni namgwirira ntchito zake zonse.


Ndipo tsono munditumizire munthu waluso lakuchita ndi golide, ndi siliva, ndi mkuwa, ndi chitsulo, ndi thonje lofiirira, ndi lofiira, ndi lamadzi, wakudziwa kuzokota zozokota zilizonse, akhale ndi amuna aluso okhala ndi ine mu Yuda ndi mu Yerusalemu, amene Davide atate wanga anawakonzeratu.


Ndipo uzipanga chihema ndi nsalu zophimba khumi, za bafuta wa thonje losansitsa, ndi thonje lamadzi, ndi lofiirira, ndi lofiira; uombemo akerubi, ntchito ya mmisiri.


Upangenso chapachifuwa cha chiweruzo, ntchito ya mmisiri; uchiombe mwa chiombedwe cha efodi; uchiombe ndi golide, lamadzi, ndi lofiirira, ndi lofiira, ndi bafuta wa thonje losansitsa.


ndipo ndamdzaza ndi mzimu wa Mulungu, ndi luso, ndi nzeru, ndi chidziwitso, ndi m'ntchito zilizonse,


ndi kuzokota miyala yoikika, ndi kozokota mtengo, kuchita ntchito zilizonse.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa