ndi pa mbali yake ina ya chihema, mbali ya kumpoto, pakhale matabwa makumi awiri; ndi makamwa asiliva makumi anai;
Eksodo 26:21 - Buku Lopatulika makamwa awiri pansi pa thabwa limodzi, ndi makamwa awiri pansi pa thabwa lina. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 makamwa awiri pansi pa thabwa limodzi, ndi makamwa awiri pansi pa thabwa lina. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa ndi masinde makumi anai asiliva, aŵiri pa fulemu lililonse. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Upangenso matsinde 40 asiliva, awiri pansi pa feremu iliyonse. |
ndi pa mbali yake ina ya chihema, mbali ya kumpoto, pakhale matabwa makumi awiri; ndi makamwa asiliva makumi anai;
Ndipo matalente zana limodzi a siliva ndiwo a kuyengera makamwa a malo opatulika, ndi makamwa a nsalu yotchinga; makamwa zana limodzi matalente zana limodzi, talente limodzi kamwa limodzi.