Eksodo 26:21 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Upangenso matsinde 40 asiliva, awiri pansi pa feremu iliyonse. Onani mutuwoBuku Lopatulika21 makamwa awiri pansi pa thabwa limodzi, ndi makamwa awiri pansi pa thabwa lina. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 makamwa awiri pansi pa thabwa limodzi, ndi makamwa awiri pansi pa thabwa lina. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 ndi masinde makumi anai asiliva, aŵiri pa fulemu lililonse. Onani mutuwo |