Eksodo 26:20 - Buku Lopatulika20 ndi pa mbali yake ina ya chihema, mbali ya kumpoto, pakhale matabwa makumi awiri; ndi makamwa asiliva makumi anai; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 ndi pa mbali yake ina ya Kachisi, mbali ya kumpoto, pakhale matabwa makumi awiri; ndi makamwa asiliva makumi anai; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Ndipo kumpoto kwa chihemacho upangenso mafulemu makumi aŵiri, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Ndipo mbali yakumpoto ya chihemacho upangenso maferemu makumi awiri. Onani mutuwo |