ndi zikopa za nkhosa zamphongo zonyika zofiira, ndi zikopa za akatumbu, ndi mtengo wakasiya;
Eksodo 26:15 - Buku Lopatulika Ndipo uzipangira chihema matabwa oimirika, a mtengo wakasiya. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo uzipangira Kachisi matabwa oimirika, a mtengo wakasiya. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa “Upange mafulemu a chihemacho ndi matabwa oimirira bwino a mtengo wa kasiya. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero “Upange maferemu amatabwa amtengo wa mkesha oyimikira chihemacho. |
ndi zikopa za nkhosa zamphongo zonyika zofiira, ndi zikopa za akatumbu, ndi mtengo wakasiya;
Utali wake wa thabwa limodzi ndiwo mikono khumi, ndi kupingasa kwake kwa thabwali mkono ndi hafu.