Amenewo ndiwo mau walamulira Yehova, Aoleko yense monga mwa njala yake; munthu mmodzi omeri limodzi, monga momwe muli, yense atengere iwo m'hema mwake.
Eksodo 16:36 - Buku Lopatulika Koma omeri ndilo limodzi la magawo khumi la efa. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Koma omeri ndilo limodzi la magawo khumi la efa. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Malita aŵiri alingana ndi gawo lachikhumi la efa. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero (Malita awiri amafanana ndi gawo lakhumi la efa). |
Amenewo ndiwo mau walamulira Yehova, Aoleko yense monga mwa njala yake; munthu mmodzi omeri limodzi, monga momwe muli, yense atengere iwo m'hema mwake.
Efa ndi bati zikhale za muyeso umodzi, bati liyese limodzi la magawo khumi la homeri, efa lomwe liyese limodzi la magawo khumi la homeri; muyeso wao uyesedwa monga mwa homeri.
ndi limodzi la magawo khumi la efa wa ufa wosalala ukhale nsembe yaufa, wosakaniza ndi limodzi la magawo anai la hini wa mafuta opera.
Natola khunkha iye m'munda mpaka madzulo; naomba khunkhalo; napeza ngati efa wa barele,