Rute 2:17 - Buku Lopatulika17 Natola khunkha iye m'munda mpaka madzulo; naomba khunkhalo; napeza ngati efa wa barele, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Natola khunkha iye m'munda mpaka madzulo; naomba khunkhalo; napeza ngati efa wa barele, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Choncho Rute adakunkha m'mundamo mpaka madzulo. Pambuyo pake adapuntha barele amene adakunkha uja, ndipo adakwanira pafupi makilogramu khumi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Choncho Rute anakunkha mʼmundamo mpaka madzulo. Kenaka anapuntha barele anakunkhayo, ndipo anakwanira pafupifupi makilogalamu khumi. Onani mutuwo |