Numeri 28:5 - Buku Lopatulika5 ndi limodzi la magawo khumi la efa wa ufa wosalala ukhale nsembe yaufa, wosakaniza ndi limodzi la magawo anai la hini wa mafuta opera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 ndi limodzi la magawo khumi la efa wa ufa wosalala ukhale nsembe yaufa, wosanganiza ndi limodzi la magawo anai la hini wa mafuta opera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Muziperekanso kilogaramu limodzi la ufa wosalala, wosakaniza ndi mafuta aolivi oyenga bwino okwanira lita limodzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Muziperekanso kilogalamu imodzi ya ufa wosalala wosakaniza ndi lita imodzi ya mafuta a olivi. Onani mutuwo |