Eksodo 16:35 - Buku Lopatulika35 Ndipo ana a Israele anadya mana zaka makumi anai, kufikira atalowa dziko la midzi; anadya mana kufikira analowa malire a dziko la Kanani. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201435 Ndipo ana a Israele anadya mana zaka makumi anai, kufikira atalowa dziko la midzi; anadya mana kufikira analowa malire a dziko la Kanani. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa35 Aisraelewo adakhala alikudya mana zaka makumi anai, mpaka adakafika kudziko kokhala anthu. Adadya mana mpaka adafika ku malire a dziko la Kanani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero35 Aisraeli anadya mana zaka 40, mpaka pamene anafika ku dziko kumene amati akakhazikeko. Iwo anadya mana mpaka pamene anafika mʼmalire a Kanaani. Onani mutuwo |