Eksodo 16:36 - Buku Lopatulika36 Koma omeri ndilo limodzi la magawo khumi la efa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201436 Koma omeri ndilo limodzi la magawo khumi la efa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa36 Malita aŵiri alingana ndi gawo lachikhumi la efa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero36 (Malita awiri amafanana ndi gawo lakhumi la efa). Onani mutuwo |