Eksodo 16:34 - Buku Lopatulika34 Monga Yehova analamula Mose, momwemo Aroni anauika patsogolo pa Mboni, usungikeko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Monga Yehova anauza Mose, momwemo Aroni anauika patsogolo pa Mboni, usungikeko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Monga momwe Chauta adalamulira Mose, Aroni adaika mtsukowo patsogolo pa bokosi lachipangano, kuti manayo asungike. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Monga momwe Yehova analamulira Mose, Aaroni anayika mtsuko uja pafupi ndi bokosi la Chipangano kuti manawo asungike. Onani mutuwo |