Eksodo 16:33 - Buku Lopatulika33 Ndipo Mose anati kwa Aroni, Tenga mphika, nuthiremo mana odzala omeri, nuuike pamaso pa Yehova, usungikire mibadwo yanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201433 Ndipo Mose anati kwa Aroni, Tenga mphika, nuthiremo mana odzala omeri, nuuike pamaso pa Yehova, usungikire mibadwo yanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa33 Ndipo Mose adauza Aroni kuti, “Tenga mtsuko, uikemo mana wokwana malita aŵiri. Utatero uike pamaso pa Chauta kuti manayo asungike chifukwa cha zidzukulu zanu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero33 Choncho Mose anati kwa Aaroni, “Tenga mtsuko ndipo uyikemo malita awiri a mana. Ndipo uyike manawo pamaso pa Yehova kusungira mibado imene ikubwera.” Onani mutuwo |