Koma sanammvere Mose; ndipo ena anasiyako kufikira m'mawa; koma unagwa mphutsi, nununkha. Ndipo Mose anakwiya nao.
Eksodo 16:24 - Buku Lopatulika Ndipo anausunga kufikira m'mawa, monga adalamulira Mose; koma sunanunkhe, ndipo sunagwe mphutsi. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anausunga kufikira m'mawa, monga adalamulira Mose; koma sunanunkha, ndipo sunagwa mphutsi. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mose atalamula zimenezi, anthuwo adasungadi totsalato mpaka m'maŵa mwake tosaonongeka, ndipo sitidagwe mphutsi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Choncho anasunga mpaka mmawa monga Mose anawalamulira, ndipo sananunkhe kapena kuchita mphutsi. |
Koma sanammvere Mose; ndipo ena anasiyako kufikira m'mawa; koma unagwa mphutsi, nununkha. Ndipo Mose anakwiya nao.
Ndipo Mose anati, Muudye lero; pakuti lero ndilo Sabata la Yehova; simuupeza lero pabwalo.
Ndipo Mose anati kwa Aroni, Tenga mphika, nuthiremo mana odzala omeri, nuuike pamaso pa Yehova, usungikire mibadwo yanu.