Eksodo 16:25 - Buku Lopatulika25 Ndipo Mose anati, Muudye lero; pakuti lero ndilo Sabata la Yehova; simuupeza lero pabwalo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ndipo Mose anati, Muudye lero; pakuti lero ndilo Sabata la Yehova; simuupeza lero pabwalo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Pambuyo pake Mose adauza anthuwo kuti, “Idyani ameneyu lero, chifukwa lero ndi tsiku la Sabata loperekedwa kwa Chauta. Lero simumpezatu kunjaku. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Mose anati, “Idyani lero chifukwa lero ndi Sabata la Yehova. Lero simukapeza chilichonse kunjaku. Onani mutuwo |