Eksodo 16:24 - Buku Lopatulika24 Ndipo anausunga kufikira m'mawa, monga adalamulira Mose; koma sunanunkhe, ndipo sunagwe mphutsi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Ndipo anausunga kufikira m'mawa, monga adalamulira Mose; koma sunanunkha, ndipo sunagwa mphutsi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Mose atalamula zimenezi, anthuwo adasungadi totsalato mpaka m'maŵa mwake tosaonongeka, ndipo sitidagwe mphutsi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Choncho anasunga mpaka mmawa monga Mose anawalamulira, ndipo sananunkhe kapena kuchita mphutsi. Onani mutuwo |