Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 16:26 - Buku Lopatulika

26 Muziola uwu masiku asanu ndi limodzi; koma tsiku lachisanu ndi chiwiri ndilo la Sabata, pamenepo padzakhala palibe.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

26 Muziola uwu masiku asanu ndi limodzi; koma tsiku lachisanu ndi chiwiri ndilo la Sabata, pamenepo padzakhala palibe.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

26 Mutole chakudya pa masiku asanu ndi limodzi. Koma pa tsiku lachisanu ndi chiŵiri, tsiku la Sabata, chakudyacho sichidzapezeka.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

26 Muzitola chakudya masiku asanu ndi limodzi koma tsiku la chisanu ndi chiwiri ndi la Sabata, simukapeza chilichonse kunjaku.”

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 16:26
6 Mawu Ofanana  

Ndipo Mose anati, Muudye lero; pakuti lero ndilo Sabata la Yehova; simuupeza lero pabwalo.


Ndipo kunali tsiku la Sabata, kuti anthu ena anatuluka kukaola, koma sanaupeze.


Atero Ambuye Yehova, Pa chipata cha bwalo lam'kati choloza kum'mawa patsekedwe masiku asanu ndi limodzi ogwira ntchito; koma tsiku la Sabata patsegulidwe, ndi tsiku lokhala mwezi patsegulidwe.


Ndipo mkulu wa sunagoge anavutika mtima, chifukwa Yesu anachiritsa tsiku la Sabata, nayankha, nanena kwa khamulo, Alipo masiku asanu ndi limodzi, m'menemo anthu ayenera kugwira ntchito, chifukwa chake idzani kudzachiritsidwa momwemo, koma tsiku la Sabata ai.


Masiku asanu ndi limodzi uzigwiritsa ntchito, ndi kuchita ntchito zako zonse;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa