Eksodo 16:27 - Buku Lopatulika27 Ndipo kunali tsiku la Sabata, kuti anthu ena anatuluka kukaola, koma sanaupeze. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Ndipo kunali tsiku la Sabata, kuti anthu ena anatuluka kukaola, koma sanaupeze. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Pa tsiku lachisanu ndi chiŵirilo anthu ena adaapita kuti akatole chakudya, koma sadachipeze. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Komabe anthu ena anapita kuti akatole chakudya tsiku lachisanu ndi chiwiri, koma sanapeze kanthu. Onani mutuwo |