Ndipo wokhalamo sadzanena, Ine ndidwala; anthu okhala m'menemo, adzakhululukidwa mphulupulu zao.
Eksodo 12:45 - Buku Lopatulika Mlendo kapena wolembedwa ntchito asadyeko. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Mlendo kapena wolembedwa ntchito asadyeko. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mlendo kapena wantchito wanu aliyense asadyeko. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Koma amene mukukhala naye kwa kanthawi kapena waganyu asadye Paska. |
Ndipo wokhalamo sadzanena, Ine ndidwala; anthu okhala m'menemo, adzakhululukidwa mphulupulu zao.
Mlendo asadyeko chopatulikacho; wakungokhala, ndi wansembe, kapena wolembedwa ntchito, asadyeko chopatulikacho.
kuti nthawi ija munali opanda Khristu, alendo a padera ndi mbumba ya Israele, ndi alendo alibe kanthu ndi mapangano a malonjezano, opanda chiyembekezo, ndi opanda Mulungu m'dziko lapansi.