Eksodo 12:46 - Buku Lopatulika46 Audye m'nyumba imodzi; usatulukira nayo kubwalo nyama ina; ndipo musathyole fupa lake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201446 Audye m'nyumba imodzi; usatulukira nayo kubwalo nyama ina; ndipo musathyole fupa lake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa46 Muzidyera m'nyumba imodzi, musatuluke nayo panja nyamayo, ndipo musaphwanye mafupa ake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero46 “Muzidyera Paska mʼnyumba imodzi. Musatulutse nyama iliyonse kunja kwa nyumba. Musaswe mafupa aliwonse. Onani mutuwo |