Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 12:47 - Buku Lopatulika

47 Gulu lonse la Israele lizichita ichi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

47 Msonkhano wonse wa Israele uzichita ichi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

47 Mtundu wonse wa Aisraele uzichita mwambo umenewu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

47 Gulu lonse la Israeli lizichita mwambo wachikondwererochi.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 12:47
4 Mawu Ofanana  

Mulankhule ndi gulu lonse la Israele ndi kuti, Tsiku lakhumi la mwezi uno adzitengere munthu yense mwanawankhosa, monga mwa mabanja a atate ao, mwanawankhosa pabanja.


Ndipo mukhale naye chisungire kufikira tsiku lakhumi ndi chinai la mwezi womwe; ndipo gulu lonse la Israele lizamuphe madzulo.


Munthu akakhala woyera, wosakhala paulendo, koma akaleka kuchita Paska, amsadze munthuyo kwa anthu a mtundu wake; popeza sanabwere nacho chopereka cha Yehova pa nyengo yake yoikidwa, munthuyu asenze kuchimwa kwake.


Ndipo mlendo akakhala mwa inu, nakachitira Yehova Paska, azichita monga mwa lemba la Paska, ndi monga mwa chiweruzo chake; lemba likhale limodzi kwa inu, ndi kwa mlendo, ndi kwa wobadwa m'dziko.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa