Ndipo tsopano Ambuye, penyani mau ao akuopsa, ndipo patsani kwa akapolo anu alankhule mau anu ndi kulimbika mtima konse,
Akolose 4:4 - Buku Lopatulika kuti ndichionetse ichi monga ndiyenera kulankhula. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 kuti ndichionetse ichi monga ndiyenera kulankhula. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mundipempherere tsono kuti ndichifotokoze bwino monga ndiyenera. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pempherani kuti ndilalikire momveka bwino, monga ndikuyenera. |
Ndipo tsopano Ambuye, penyani mau ao akuopsa, ndipo patsani kwa akapolo anu alankhule mau anu ndi kulimbika mtima konse,
chifukwa cha umene ndili mtumiki wa mu unyolo, kuti m'menemo ndikalankhule molimbika, monga ndiyenera kulankhula.
Mau anu akhale m'chisomo, okoleretsa, kuti mukadziwe inu mayankhidwe anu a kwa yense akatani.