Akolose 4:5 - Buku Lopatulika5 Muyendere munzeru ndi iwo akunja, kuchita machawi nthawi ingatayike. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Muyendere munzeru ndi iwo akunja, kuchita machawi nthawi ingatayike. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Mayendedwe anu pakati pa anthu akunja azikhala anzeru, ndipo muzichita changu, osataya nthaŵi pachabe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Mayendedwe anu pakati pa akunja, akhale anzeru ndipo mugwiritse ntchito mpata uliwonse umene muli nawo. Onani mutuwo |