2 Akorinto 3:12 - Buku Lopatulika12 Pokhala nacho tsono chiyembekezo chotere, tilankhula ndi kukhazikika mtima kwakukulu, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Pokhala nacho tsono chiyembekezo chotere, tilankhula ndi kukhazikika mtima kwakukulu, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Popeza kuti timayembekeza zimenezi, timalimba mtima kwambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Choncho, popeza tili ndi chiyembekezo chotere, ndife olimba mtima kwambiri. Onani mutuwo |