2 Akorinto 3:13 - Buku Lopatulika13 ndipo si monga Mose, amene anaika chophimba pa nkhope yake, kuti ana a Israele asayang'anitse pa chimaliziro cha chimene chinalikuchotsedwa; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 ndipo si monga Mose, amene anaika chophimba pa nkhope yake, kuti ana a Israele asayang'anitse pa chimaliziro cha chimene chinalikuchotsedwa; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Sitichita ngati Mose amene ankaphimba nkhope yake ndi nsalu, kuwopa kuti Aisraele angamapenye kutha kwake kwa kuŵala kosakhalitsa kuja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Ife sitili ngati Mose amene amaphimba nkhope yake kuopa kuti Aisraeli angaone kuti kunyezimira kwa nkhope yake kumazilala. Onani mutuwo |