2 Akorinto 3:11 - Buku Lopatulika11 Pakuti ngati chimene chilikuchotsedwa chinakhala mu ulemerero, makamaka kwambiri chotsalacho chili mu ulemerero. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Pakuti ngati chimene chilikuchotsedwa chinakhala m'ulemerero, makamaka kwambiri chotsalacho chili m'ulemerero. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Tsono ngati zinthu zosakhalitsa zidaafika ndi ulemerero, ndiye kuti zinthu zokhala mpaka muyaya zidzakhala ndi ulemerero wopambana. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Ndipo ngati zosakhalitsa zinabwera ndi ulemerero, koposa kotani ulemerero wamuyayawo! Onani mutuwo |