2 Akorinto 3:10 - Buku Lopatulika10 Pakutinso chimene chinachitidwa cha ulemerero sichinachitidwe cha ulemerero m'menemo, chifukwa cha ulemerero woposawo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Pakutinso chimene chinachitidwa cha ulemerero sichinachitidwa cha ulemerero m'menemo, chifukwa cha ulemerero woposawo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Chifukwa cha ulemerero wopambanawu umene waoneka tsopano, zinthu zimene kale zidaali ndi ulemerero, masiku ano zilibenso ulemerero konse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Pakuti zimene zinali ndi ulemerero, tsopano zilibenso ulemerero pofananitsa ndi ulemerero wopambanawo. Onani mutuwo |