2 Akorinto 3:9 - Buku Lopatulika9 Pakuti ngati utumiki wa chitsutso unali wa ulemerero, makamaka utumiki wa chilungamo uchulukira muulemerero kwambiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Pakuti ngati utumiki wa chitsutso unali wa ulemerero, makamaka utumiki wa chilungamo uchulukira muulemerero kwambiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Ngati ntchito yoweruza anthu kuti alangidwe inali yaulemerero, ndiye kuti ntchito yoti anthu apezeke olungama pamaso pa Mulungu idzakhala yaulemerero koposa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Ngati utumiki umene umatsutsa anthu unali ndi ulemerero, nanga koposa kotani ulemerero wa utumiki wobweretsa chilungamo! Onani mutuwo |