Ahebri 11:2 - Buku Lopatulika Pakuti momwemo akulu anachitidwa umboni. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Pakuti momwemo akulu anachitidwa umboni. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pokhala ndi chikhulupiriro, makolo anthu akale aja Mulungu adaonetsa kuti ankakondwera nawo. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndi chikhulupiriro chimenechi makolo athu akale anayamikidwa. |
Ndi chikhulupiriro Abele anapereka kwa Mulungu nsembe yoposa ija ya Kaini, imene anachitidwa umboni nayo kuti anali wolungama; nachitapo umboni Mulungu pa mitulo yake; ndipo momwemo iye, angakhale adafa alankhulabe.