2 Samueli 5:14 - Buku Lopatulika Maina a iwo anambadwira mu Yerusalemu ndi awa: Samuwa, ndi Sobabu, ndi Natani, ndi Solomoni, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Maina a iwo anambadwira m'Yerusalemu ndi awa: Samuwa, ndi Sobabu, ndi Natani, ndi Solomoni, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Naŵa maina a ana a Davide amene adabadwira ku Yerusalemu: Samuwa, Sobabu, Natani, Solomoni, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mayina a ana amene anabereka ku Yerusalemu ndi awa: Samua, Sobabu, Natani, Solomoni, |
ndi Azariya mwana wa Natani anayang'anira akapitao, ndipo Zabudi mwana wa Natani anali wansembe ndi nduna yopangira mfumu,
Ndipo dziko lidzalira, banja lililonse pa lokha; banja la nyumba ya Davide pa lokha, ndi akazi ao pa okha; banja la nyumba ya Natani pa lokha, ndi akazi ao pa okha;