Mateyu 1:6 - Buku Lopatulika6 ndi Yese anabala Davide mfumuyo. Ndipo Davide anabala Solomoni mwa mkazi wa Uriya; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 ndi Yese anabala Davide mfumuyo. Ndipo Davide anabala Solomoni mwa mkazi wa Uriya; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Yese adabereka mfumu Davide. Davide adabereka Solomoni, mwa amene poyamba adaali mkazi wa Uriya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Yese anabereka Mfumu Davide. Ndipo Davide anabereka Solomoni, amene amayi ake anali mkazi wa Uriya. Onani mutuwo |