Mateyu 1:5 - Buku Lopatulika5 ndi Salimoni anabala Bowazi mwa Rahabu; ndi Bowazi anabala Obede mwa Rute; ndi Obede anabala Yese; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 ndi Salimoni anabala Bowazi mwa Rahabu; ndi Bowazi anabala Obede mwa Rute; ndi Obede anabala Yese; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Salimoni adabereka Bowazi mwa Rahabu, Bowazi adabereka Obede mwa Rute, Obede adabereka Yese, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Salimoni anabereka Bowazi amene amayi ake anali Rahabe, Bowazi anabereka Obedi amene amayi ake anali Rute, Obedi anabereka Yese. Onani mutuwo |