2 Samueli 5:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo Davide anadzitengera akazi aang'ono ena ndi akazi a ulemu ena a ku Yerusalemu, atafikako kuchokera ku Hebroni; ndipo anambadwira Davide ana aamuna ndi aakazi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo Davide anadzitengera akazi aang'ono ena ndi akazi a ulemu ena a ku Yerusalemu, atafikako kuchokera ku Hebroni; ndipo anambadwira Davide ana aamuna ndi aakazi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Tsono Davide atafika ku Yerusalemu kuchokera ku Hebroni, adakwatira akazi ena natenganso azikazi ena kumeneko. Tsono adabereka ana ambiri, aamuna ndi aakazi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Davide atafika ku Yerusalemu kuchokera ku Hebroni, anakwatira azikazi natenganso akazi ena kumeneko, ndipo anabereka ana aamuna ndi aakazi ambiri. Onani mutuwo |