2 Samueli 5:14 - Buku Lopatulika14 Maina a iwo anambadwira mu Yerusalemu ndi awa: Samuwa, ndi Sobabu, ndi Natani, ndi Solomoni, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Maina a iwo anambadwira m'Yerusalemu ndi awa: Samuwa, ndi Sobabu, ndi Natani, ndi Solomoni, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Naŵa maina a ana a Davide amene adabadwira ku Yerusalemu: Samuwa, Sobabu, Natani, Solomoni, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Mayina a ana amene anabereka ku Yerusalemu ndi awa: Samua, Sobabu, Natani, Solomoni, Onani mutuwo |