kuchotsa ufumu kunyumba ya Saulo ndi kukhazika mpando wachifumu wa Davide pa Israele ndi pa Yuda, kuyambira ku Dani kufikira ku Beereseba.
2 Samueli 3:11 - Buku Lopatulika Ndipo iye sanakhoze kuyankha Abinere mau amodzi chifukwa cha kumuopa iye. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo iye sanakhoze kuyankha Abinere mau amodzi chifukwa cha kumuopa iye. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pamenepo Isiboseti adangoti kukamwa yasa, osatha kumuyankha Abinere mau ndi amodzi omwe, chifukwa ankamuwopa kwambiri. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Isiboseti sanayerekezenso kunena mawu ena kwa Abineri, chifukwa ankamuopa. |
kuchotsa ufumu kunyumba ya Saulo ndi kukhazika mpando wachifumu wa Davide pa Israele ndi pa Yuda, kuyambira ku Dani kufikira ku Beereseba.
Ndipo Abinere anatuma mithenga imnenere kwa Davide, nati, Dziko nla yani? Natinso, Mupangane nane pangano lanu, ndipo onani, ndidzagwirizana nanu ndi kukopa Aisraele onse atsate inu.