2 Samueli 22:13 - Buku Lopatulika Cheza cha pamaso pake makala a moto anayaka. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Cheza cha pamaso pake makala a moto anayaka. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa M'kuŵala kumene kunali pamaso pake munkafumira makala amoto alaŵilaŵi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mʼkuwala kumene kunali pamaso pake munkachokera makala amoto alawilawi. |
M'mphuno mwake munatuluka utsi, ndi moto wotuluka m'kamwa mwake unaononga; makala anayaka nao.
Ndipo maonekedwe a ulemerero wa Yehova anali ngati moto wonyeketsa pamwamba paphiri, pamaso pa ana a Israele.