Mfumu nituluka, ndi banja lake lonse linamtsata. Ndipo mfumu inasiya akazi khumi ndiwo akazi aang'ono, kusunga nyumbayo.
2 Samueli 15:17 - Buku Lopatulika Ndipo mfumu inatuluka, ndi anthu onse anamtsata; naima kunyumba ya pa yokha. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo mfumu inatuluka, ndi anthu onse anamtsata; naima kunyumba ya pa yokha. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pamene mfumu idatuluka, anthu onse adaitsata. Onsewo adakaima pa nyumba yomalizira. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Kotero mfumu inanyamuka pamodzi ndi anthu onse oyitsatira, ndipo anayima pamalo pena chapatalipo. |
Mfumu nituluka, ndi banja lake lonse linamtsata. Ndipo mfumu inasiya akazi khumi ndiwo akazi aang'ono, kusunga nyumbayo.
Ndipo anyamata ake onse anapita naye limodzi; ndi Akereti ndi Apeleti, ndi Agiti onse, anthu mazana asanu ndi limodzi omtsata kuchokera ku Gati, anapita pamaso pa mfumu.
Munapititsa anthu oberekeka pamwamba pamitu pathu; tinapyola moto ndi madzi; koma munatifikitsa potitsitsimutsa.