2 Samueli 15:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo anyamata ake onse anapita naye limodzi; ndi Akereti ndi Apeleti, ndi Agiti onse, anthu mazana asanu ndi limodzi omtsata kuchokera ku Gati, anapita pamaso pa mfumu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo anyamata ake onse anapita naye limodzi; ndi Akereti ndi Apeleti, ndi Agiti onse, anthu mazana asanu ndi limodzi omtsata kuchokera ku Gati, anapita pamaso pa mfumu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Ankhondo ake onse adayamba kuyenda pamaso pa Davide, ndipo Akereti ndi Apeleti kudzanso Agiti okwanira 600 amene adamtsata kuchokera ku Gati, nawonso adayenda pamaso pa mfumu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Ankhondo ake onse anayamba kuyenda pamaso pa Davide, ndipo Akereti ndi Apeleti, pamodzinso ndi Agiti okwanira 600 amene anamutsata kuchokera ku Gati, nawonso anayenda pamaso pake. Onani mutuwo |