2 Samueli 15:17 - Buku Lopatulika17 Ndipo mfumu inatuluka, ndi anthu onse anamtsata; naima kunyumba ya pa yokha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Ndipo mfumu inatuluka, ndi anthu onse anamtsata; naima kunyumba ya pa yokha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Pamene mfumu idatuluka, anthu onse adaitsata. Onsewo adakaima pa nyumba yomalizira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Kotero mfumu inanyamuka pamodzi ndi anthu onse oyitsatira, ndipo anayima pamalo pena chapatalipo. Onani mutuwo |