2 Samueli 15:16 - Buku Lopatulika16 Mfumu nituluka, ndi banja lake lonse linamtsata. Ndipo mfumu inasiya akazi khumi ndiwo akazi aang'ono, kusunga nyumbayo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Mfumu nituluka, ndi banja lake lonse linamtsata. Ndipo mfumu inasiya akazi khumi ndiwo akazi aang'ono, kusunga nyumbayo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Choncho mfumu idatuluka, nipita pamodzi ndi anthu onse a pabanja pake. Koma mfumuyo idasiya azikazi ake khumi kuti azisunga mudzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Mfumu inanyamuka pamodzi ndi banja lake lonse. Koma iye anasiya azikazi khumi kuti azisamalira nyumba yaufumu. Onani mutuwo |