Mlaliki 10:7 - Buku Lopatulika7 Ndaona akapolo atakwera pa akavalo, ndi mafumu, alikuyenda pansi ngati akapolo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndaona akapolo atakwera pa akavalo, ndi mafumu, alikuyenda pansi ngati akopolo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Ndaona akapolo akuyenda pa akavalo, m'menemo akalonga akuyenda pansi ngati akapolo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Ndaona akapolo atakwera pa akavalo, pamene akalonga akuyenda pansi ngati akapolo. Onani mutuwo |