Pakutinso chimene chinachitidwa cha ulemerero sichinachitidwe cha ulemerero m'menemo, chifukwa cha ulemerero woposawo.
2 Akorinto 3:11 - Buku Lopatulika Pakuti ngati chimene chilikuchotsedwa chinakhala mu ulemerero, makamaka kwambiri chotsalacho chili mu ulemerero. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Pakuti ngati chimene chilikuchotsedwa chinakhala m'ulemerero, makamaka kwambiri chotsalacho chili m'ulemerero. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Tsono ngati zinthu zosakhalitsa zidaafika ndi ulemerero, ndiye kuti zinthu zokhala mpaka muyaya zidzakhala ndi ulemerero wopambana. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndipo ngati zosakhalitsa zinabwera ndi ulemerero, koposa kotani ulemerero wamuyayawo! |
Pakutinso chimene chinachitidwa cha ulemerero sichinachitidwe cha ulemerero m'menemo, chifukwa cha ulemerero woposawo.
Pakunena Iye, Latsopano, anagugitsa loyambali. Koma chimene chilinkuguga ndi kusukuluka, chayandikira kukanganuka.