2 Akorinto 4:1 - Buku Lopatulika1 Chifukwa chake popeza tili nao utumiki umene, monga talandira chifundo, sitifooka; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Chifukwa chake popeza tili nao utumiki umene, monga talandira chifundo, sitifooka; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Mulungu mwa chifundo chake adatipatsa ntchitoyi, nchifukwa chake sititaya mtima. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Choncho popeza mwachifundo cha Mulungu tili ndi utumiki uwu, sititaya mtima. Onani mutuwo |