Ndipo Iye ananena naye, Indetu, ndinena ndi iwe, Lero lino udzakhala ndine mu Paradaiso.
2 Akorinto 12:3 - Buku Lopatulika Ndipo ndidziwa munthu wotereyo (ngati m'thupi, ngati wopanda thupi, sindidziwa; adziwa Mulungu), Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo ndidziwa munthu wotereyo (ngati m'thupi, ngati wopanda thupi, sindidziwa; adziwa Mulungu), Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ndikudziŵa kuti munthuyo adaatengedwa mwadzidzidzi kupita ku Paradizo. Sindikudziŵa ngati zimenezi zidaachitika ali m'thupi, kapena ali kunja kwa thupi. Akudziŵa ndi Mulungu zimenezi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndipo ndikumudziwa munthu ameneyu. Sindikudziwa ngati zinachitika mʼthupi kapena ayi, zimenezo akudziwa ndi Mulungu. |
Ndipo Iye ananena naye, Indetu, ndinena ndi iwe, Lero lino udzakhala ndine mu Paradaiso.
Ndidziwa munthu wa mwa Khristu, zitapita zaka khumi ndi zinai (ngati m'thupi, sindidziwa; ngati kunja kwa thupi, sindidziwa; adziwa Mulungu), anakwatulidwa wotereyo kunka naye Kumwamba kwachitatu.