2 Akorinto 12:4 - Buku Lopatulika4 kuti anakwatulidwa kunka ku Paradaiso, namva maneno osatheka kuneneka, amene saloleka kwa munthu kulankhula. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 kuti anakwatulidwa kunka ku Paradaiso, namva maneno osatheka kuneneka, amene saloleka kwa munthu kulankhula. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Kumeneko munthuyo adamva zinthu zosasimbika, zinthu zimene munthu sangazilankhule. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Munthuyu anatengedwa kupita ku paradizo. Ndipo anamva zinthu zosatheka kuneneka, zinthu zimene munthu saloledwa kunena. Onani mutuwo |