2 Akorinto 12:5 - Buku Lopatulika5 Chifukwa cha wotereyo ndidzadzitamandira; koma chifukwa cha ine ndekha sindidzadzitamandira, koma m'zofooka zanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Chifukwa cha wotereyo ndidzadzitamandira; koma chifukwa cha ine ndekha sindidzadzitamandira, koma m'zofooka zanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Munthu wotere ndidzamnyadira, koma kunena za ine ndekha, sindidzanyadira kanthu kena koma kufooka kwanga kokha. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Ndidzatamanda za munthu ngati ameneyu, koma sindidzadzitamandira ine mwini kupatula za kufowoka kwanga. Onani mutuwo |