2 Akorinto 11:11 - Buku Lopatulika11 Chifukwa ninji? Chifukwa sindikonda inu kodi? Adziwa Mulungu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Chifukwa ninji? Chifukwa sindikonda inu kodi? Adziwa Mulungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Ndikutero chifukwa chiyani? Kodi monga sindikukondani? Akudziŵa ndi Mulungu kuti ndimakukondani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Nʼchifukwa chiyani ndikutero? Kodi nʼchifukwa choti sindikukondani? Mulungu akudziwa kuti ndimakukondani! Onani mutuwo |