Ndipo panali pamene Yeremiya anatha kunena kwa anthu onse mau onse a Yehova Mulungu wao, amene anamtuma iye nao Yehova Mulungu wao, mau onse amenewo,
1 Samueli 8:10 - Buku Lopatulika Ndipo Samuele anauza anthu akumpempha iye mfumu mau onse a Yehova. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Samuele anauza anthu akumpempha iye mfumu mau onse a Yehova. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Choncho Samuele adaŵauza anthu amene ankafuna mfumu aja mau onse a Chauta. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Samueli anawawuza anthu amene amamupempha mfumu aja mawu onse a Yehova. |
Ndipo panali pamene Yeremiya anatha kunena kwa anthu onse mau onse a Yehova Mulungu wao, amene anamtuma iye nao Yehova Mulungu wao, mau onse amenewo,
Nati, Awa ndi makhalidwe a mfumu imene idzaweruza inu; idzatenga ana anu aamuna, akhale akusunga magaleta, ndi akavalo ake; ndipo adzathamanga ndi kutsogolera magaleta ake;