1 Samueli 8:9 - Buku Lopatulika9 Chifukwa chake tsono umvere mau ao; koma uwachenjeze kolimba, ndi kuwadziwitsa makhalidwe ake a mfumu imene idzawaweruza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Chifukwa chake tsono umvere mau ao; koma uwachenjeze kolimba, ndi kuwadziwitsa makhalidwe ake a mfumu imene idzawaweruza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Motero tsono umvere zimene iwowo akunena. Koma ndiye uŵachenjeze kwambiri, ndipo uŵauzitse za mkhalidwe wake wa mfumu imene izidzaŵalamulirayo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Tsono amvere zimene akunena, koma uwachenjeze kwambiri ndipo uwawuzitse za khalidwe la mfumu imene idzawalamulire.” Onani mutuwo |