1 Samueli 8:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo Samuele anauza anthu akumpempha iye mfumu mau onse a Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo Samuele anauza anthu akumpempha iye mfumu mau onse a Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Choncho Samuele adaŵauza anthu amene ankafuna mfumu aja mau onse a Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Samueli anawawuza anthu amene amamupempha mfumu aja mawu onse a Yehova. Onani mutuwo |